(TINGOSEKAKO PANGONO) MAN ENA AKE ANAMWALIRA NDIPO ANAPITA - TopicsExpress



          

(TINGOSEKAKO PANGONO) MAN ENA AKE ANAMWALIRA NDIPO ANAPITA KUMWAMBA atafika pakhomo lopapatiza anawona ma wotchi apakhoma ochuluka heavy pafupi ndi iye.Ndipo anafunsa mawotchi osewa achani? ndipo paulo woyela anayankha awa ndi ma wotchi a momwe munthu akumanamila pa dziko lapansi,ali yense ali ndi wotchi yake ya mmene wanamila, panthawi yomwe munthu wangonama,ka muvi kamayenda. man aja anayankha oky! Zimakhala choncho ndiye wotchi ili apoyo ndiyandan? paulo anayankha: ndiya mayi maria imeneyo ndipo ka muviko sikanayendepo kusonyeza kut sanapangepo bodza. man: zosangalatsa ndithu,nanga iyo ndiyandan? Paulo: ndiya lev imeneyo ndipo kamuviko kayenda kawiri, kusonyeza kut wanama kawiri kokha basi. MAN: ndiye ma wotchi ama president akumalawi ali kut.Ndipo paulo anayankha,ali mu office tikuwagwilitsa ntchito ngat ma ceiling fan(coz amanama kwambiri)
Posted on: Fri, 24 Oct 2014 05:50:44 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015