ZIFUKWA ZIMENE A MALAWI AKUKANIRA KUTI NORTHERN REGION ISAKHALA - TopicsExpress



          

ZIFUKWA ZIMENE A MALAWI AKUKANIRA KUTI NORTHERN REGION ISAKHALA YOZIYIMILA PA YOKHA 1. Ma lecturer ambiri aku University of Malawi amachokera ku North ndiye kuti abwelere pavuta. UNIMA yonse umphawi. 2. Anthu ambiri ali ku Johannesburg are from the North. Ndiye forex kwambiri timadalira iwo 3. The North has Songwe boarder which brings along the highest collection of custom revenues 4. Ku nkhani ya chakudya, the North ili pa number 2, pa no. 1 pali Central Region. The north and centre feed Malawi. Apart from 2013, munamvapo kuti ku North kuli njala? 5. Ma chick abwino, anthu ophunzira, anthu ozindikila ali kumeneku. Kodi Goodal Gondwe ngwakuti? 6. Mukamapita ku Tanzania mumadzera kuti? Nanga mukamakatenga galimoto zowoda ku beforward mumakatengera through kuti? 7. With Kayelekera mine, Nyika mine, Mchenga Coal Mine, the north contribute majority of mining revenues 8. The northern part of Lake Malawi has oil musova!!
Posted on: Wed, 24 Sep 2014 11:20:12 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015