ku Phalombe kunabwera azungu aku America.atafika mmudzi - TopicsExpress



          

ku Phalombe kunabwera azungu aku America.atafika mmudzi mmene munafela John Chilembwe anawuza anthu kuti amene angakwanitse kupeza chigaza( skull) cha John Chilembwe amupatsa $500000. Gogo wina amene amadziwa malo amene anafela John anakakumba mwachangu nkuchipeza,ndipo anampatsa ndalamayo. Patangodutsa tsiku limodzi, Mr Makasa anabwera ndi chigaza chinanso koma chochepelapo. Kukambirana kwawo kunali kotere mzungu ; tikuthandizeni bambo? Mr Makasa; eeya,ndabweretsa chigaza cha John chija.(uku akuchitulutsa) mzungu; ah,koma chabwera kaletu..komanso ichi chikuchepa! Mr Makasa; ngakhale chabwera kale, ichinso ndi cha Chilembwe yemweyo koma ali mwana..... Mzungu fainted
Posted on: Tue, 02 Dec 2014 04:24:40 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015