Admin hide my id, Post ths AsAp Ndakhala pachibwezi kwa zaka - TopicsExpress



          

Admin hide my id, Post ths AsAp Ndakhala pachibwezi kwa zaka 4, chaka cha chitatu ndinayamba kumunamiza wa chikondi wanga chifukwa cha kufooka kwanga, kenaka anapezeka kuti amalota maloto osiyanasiyana ndiku mandiuza, zokhuzana ndikuti ndikumupusisa koma ine ndi mkakana, mpaka la chi forty litakwana ndi pomwe ndinagwidwa, komano pano chikuvuta ndi chakuti mwamunayi ndimazembelerana nayeyu akumamutumizira chibwezi changachi ma mesg omamuuza kuti tikuzembeleranabe pomwe ine ndinasiya, komanso mwamuna wangayi zimenezi zikumamudwalisa, chonde amalawi zotukwanizana sizithandiza, ijst nid help.
Posted on: Sat, 29 Jun 2013 07:24:32 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015