Ena mwama Technical College amene alolezedwa ndi Boma kuyamba - TopicsExpress



          

Ena mwama Technical College amene alolezedwa ndi Boma kuyamba kuphunzitsa ma degree awo awo: 1-Andiamo Technical 2-Soche Technical 3-Salima Technical 4-Miracle Technical 5-Mzuzu Technical 6-Lilongwe Technical 7-Stephanos Vocational Training 8-Comboni Technical 9-Macoha Vocational Training 10-DAPP Mikolongwe Vocational Training 11-Don Bosco Technical 12-Namitete Technical 13-Nasawa Technical 14-Mitengo Technical 15-Mphwezi Rural Polytechnic 16-SOS Vocational Training 17-St John Paul II Leadership and IT Institute hahahahaha apapa ndiye Bachelors Degree yatha fasho, wina aliyense azikhala nayo, kukhonza 35 points uzipanga Bachelors Degree choncho sizikufunika kuyifera kwenikweni pa MSCE ayi. The only advantage of this is that ma college/university a priuate samakweza fees kawirikawiri aziziwa kuti akakweza anthu azipita ku Technical koma kuyipa kwa Degree yaku Technical ndikoti ngati salemba maphunzitsi oyiziwa ntchito, amene akuphunzitsa panowa sangamaphunzitse zenizeni angamangoyendera waponda thope wamwa.
Posted on: Sun, 24 Aug 2014 13:38:34 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015