Kwame munali kunja ndipo mwabwera kumene, anthu oyimba awa anatha - TopicsExpress



          

Kwame munali kunja ndipo mwabwera kumene, anthu oyimba awa anatha fasho kumalawi kuno ndipo angotsala dzina lokha, anagulukilatu mano basi.... 1. Josephy tembo and Grace chinga 2. Che nkhumba awa ndiwo mau anga thomasi chibade 3. Ben michael 4. Limbani banda 5. Njati mnjedede 6. Mandede pa shoprite 7. Anna matumbi 8. Wendy halawa 9. Nyasa guluzi 10._____? Note: gwaladi postion yake akuichitabe maintain...
Posted on: Tue, 24 Sep 2013 11:17:46 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015