MWANA YU NDE NDITANI NAYE - MUSSA JONASI Bambo Mussa Jonasi - TopicsExpress



          

MWANA YU NDE NDITANI NAYE - MUSSA JONASI Bambo Mussa Jonasi omwe adali paulendo opita ku Limbe kukashopa katundu wogulitsa ndipo amachokera ku Mangochi zawawonekera pamene mzimayi wina wawasiyila kamwana ka khanda osawonekanso kumene wapiti. Malinga ndi mmene zidakhalira, a Jonasi adakhala seat imodzi ndi mayi wa mwanayo yemwe adakwelera minibus yake pa Nyungwe Girls ku Chiradzulu. Atafika pa Mbulumbuzi, mzimayi wamwanayo adawapempha a Jonasi kuti awagwilire mwana yo pamene amafuna kugula tomato, koma mayiyo sadabwelenso mu minibus mo. Ndiye a Jonasi amangoti mwini mayi uja wakwera ali kumbuyo ku osaziwa kuti watsika. Tsoka ilo kamwana kanayamba kulira ndipamenetu a Jonasi amadziwa kuti khala ngati awasiyira mwana ndiye mutu wawo udazungulira kusowa mtengo ogwira. Moti panopa mwana yu amusiya pa Police ya pa Njuli. A Jonasi wonso awatsitsira limodzi. Zosakhala bwinotu zimene fanzi
Posted on: Fri, 04 Jul 2014 06:00:00 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015