Mtsikana wina ka mdima katagwa anatenga madzi ulendo - TopicsExpress



          

Mtsikana wina ka mdima katagwa anatenga madzi ulendo wakubafa kukasamba. Atangoika beseni pansi, sopo anamugwera, chifukwa cha mdima sanatopa wafufuza kwagwa sopo, anangotuluka mbafa kukatenga moto kuti awunikire uko wagwera. Chongolowa mbafa ndi moto anawona njoka itangodzikulung iza pakona la bafa... Anathamanga kuwuza wanthu ndipo posakhalitsa anaipha... Inali njoka yowopysa koma Mulungu mngwabwino. Ali ndi njira zake. Ngakhale pangawoneke ngati palibe njira, Mulungu amapangabe njira mpaka atakwanilitsa.. Kodi uli ndi mantha kapena nkhawa ndi momwe moyo wako ukuyendera kapena momwe zinthu ziliri? Mulungu akuwona zonse.... Type amen ndipo uwona Mulungu akupanga njira popanda njira....Amen!
Posted on: Wed, 05 Nov 2014 07:06:40 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015