NKHANI YOMVESA CHISONI. RIHANNA NDI CHRIS B AMWALIRA. Pamene - TopicsExpress



          

NKHANI YOMVESA CHISONI. RIHANNA NDI CHRIS B AMWALIRA. Pamene ndikunena pano ndagwidwa ndi chisoni kwambiri pamene nditamva imfa ya Rihanna ndi Chriss B omwe amwalira pangozi. Awiriwa anatengana kuti akacheze kunyanja,ndipo Rihanna chifukwa chosatha kusambira analowa pakuya ndipo Chris B yemwe ndi mamuna wake wa Rihanna analowanso pamalopo kuti amupulumutse bwezi lakelo,koma izi sizinatheke mpaka onse awiri kumwalira pomwepo. Rihanna Mtawali amachokera ku Mchinji pomwe Chriss Bauleni kwawo mku Dedza. Mizimu yawo iwuse mu mtendere. #Phungu
Posted on: Fri, 16 Aug 2013 19:53:36 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015