Panali banja lina lake la azungu osati la anthu, analibe mwana - TopicsExpress



          

Panali banja lina lake la azungu osati la anthu, analibe mwana ndiye azungu analimbikira mpaka mwana anamupeza koma chinamudabwisa mzungu wammuna uja ndichakuti mwana anapezeka anali osiyana khungu ndionse aja, ndiye mzungu wa mmuna anadabwa kenako alimkati mwamaganizo analingalira kuti mwana wokudayo sangapite naye kwawo ku German ndiye anaganiza zomupha ndiye mzungu ndi munthu ndiwosiyanadi iye anadikira mkazi wake agone kenako ndikumupaka mkazi wake poison bele kuti mwana uja akamazayamwa azamfe, mzungu anazizimuka atamva kuti watchito wake yemwe ndi driver alikuchipatala apange changu kupita kukamva chimene mchachitikira chifukwa iye amawona ngati wachita ngozi koma akumuuza kuti wamwa poison kufunsa mtundu wa poison akudabwa ndi poison amene anapaka pa bele la mkazi wake uja kuti aphe mwana, one word to driver.
Posted on: Thu, 27 Nov 2014 04:17:24 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015