Sometimes we ignore Gods advice and we do the opposite because we - TopicsExpress



          

Sometimes we ignore Gods advice and we do the opposite because we want to satisfy our feelings, careers, please people-friends ,relatives. God always give us signs but we ignore them.Sometimes we feel kuti mtima wathu ukukanitsitsa kuti tichite koma just because people are doing it timapangabe kuopa kuoneka osazitsata although tikudziwa kuti ndi ntchimo , we just do it for the sake of fit in the group or to make ourselves happy or kumvetsera ma feelings , kuutsanza mtima. Mapeto ake timagwa mmavuto. Mulungu aliyense amamupatsa warning pena kukugwetsa ulesi kuti usapite coz ukapanga ngozi, usachite coz uchimwa kapena zikuononga , usayankhule coz zizakutembenukira tsiku lina etc. Tiyeni tifike poti i cant do this coz i love God.I cant do that coz i want to please my God, I cant go there coz kukandichimwitsa and i dont want to disappoint my God. Kupanga ignore zilakolako zanthu nde nzeruzo zimenezo, kupanga ignore zofuna za anthu nde nzeruzo zimenzo chifukwa chiyambi cha nzeru nde kuopa Mulungu. Tikamuopa iyeyo nde kuti zina zonse Mulungu azingotiunikira kuti apa utere apo utere and so on. WHOEVER LISTEN TO GOD WILL NEVER MAKE MISTAKES. ITS MORE THAN 100 PERCENT TRUE.LETS OBEY HIS SIGNS,TISAPANGE IGNORE MA SIGNS AKE KUPEWA KUGWA MMAVUTO. Proverbs 9:10 The fear of the LORD is the beginning of wisdom, and knowledge of the Holy One is understanding
Posted on: Thu, 24 Apr 2014 00:23:42 +0000

Trending Topics



b>
significando que, mediante o evangelho, os gentios são
30px;">
TODAYS THOUGHT - YOUR SPOUSE & KIDS COME FIRST. Sometimes we
Choose any 3 ASSORTED items for only 999php!!! Choose any 3

Recently Viewed Topics




© 2015