Suleman Atupele Chitera: Malemu Bingu wa mutharika anaitanitsa - TopicsExpress



          

Suleman Atupele Chitera: Malemu Bingu wa mutharika anaitanitsa mafumu ku sanjika ndipo anawafunsa kuti azungu akuti ndigwetse ndalama ya kwacha, koma ndikagwetsa ndalama ya kwacha anthu akumudzi osaukisitsa abvutika kwambiri ndiye mafumu mukuti bwanji? Mafumu anakana kuti ayi, musagwetse, anthu kumudzi amasangalala kwambiri, lero mosaganiza ndalama inagwesedwa lero anthu kumudzi akulilira ku usi, running govt z serious business
Posted on: Thu, 20 Jun 2013 13:30:38 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015