Chiphaliwari chinamenya mdera lina pakati pa usiku. mnyumba ina - TopicsExpress



          

Chiphaliwari chinamenya mdera lina pakati pa usiku. mnyumba ina mdelaro mai wina anadzidzimuka kutulo. Anapita kuchipinda cha ana anapeza kuti ana onse anali kugona bwino lomwe. Atabwelera kuchipinda ndikuyambaso kugona anamva mau, pumira mkati mwamphamvu...! Maiyu, anadzidzimuka koma posakhalitsa anagonanso. Mau anamvekanso, Pumira mkati mwamphamvu... Maiyu sanazindikire chomwe chinali kuchitika ndipo anawona ngati zamaloto posachedwa anagonanso. Mau akulu anamvekanso mofuwula tsopano. NDIKUTI PUMIRA MKATI MWAMPHAMVU! Mai anadzuka mwachangu napumira mkati ndimphamvu. Posakhalitsa anamva fungo la utsi kuti chinachake chikuyaka. Atadzuka ndikufufuza komwe kumachokera utsi kunali kukhitchini yomwe inali yophatikizana ndi nyumba. Chimoto champhamvu chinali chitabuka. Chinali chimoto chosazimitsika. Mai anathamanga kudzutsa mwamuna wake ndi ana nathawa mnyumbamo mwachangu. Anthu ena anayesa kuzimitsa chimotocho koma sanaphule kanthu. Nyumba ndikatundu zonse zinathera pomwepo. Koma chinakomera banjalo popeza palibe anamwalira kapena kuvulara ndi motowo. Onse anali moyo. Ndichikhumbokhumbo cha Mulungu kuti aliyense anthufe tisakapse ndi moto. Koma sangatiyankhule maso ndi maso. He doesnt have to because his wake-up call is spoken to us repeatedly in his Word, the Bible. Wake up! God says to every one of us, Flee from the wrath to come Dzuka mwana wanga. It is appointed unto man once to die and after this the judgment. Jesus is coming again ... it may be today. Dont miss Gods wake-up call. Ngati sunamulandire Yesu Lets pray this prayer together: Dear God, I hear your wake up call as faint as it may be. Ndikuvomeleza ndine ochimwa ndipo ndikupempha mundikhululukire. Thank you, Jesus, for dying on the cross to pay the penalty for all my sins. I invite you to come into my heart and life as my God and my Savior. Mothandizidwa nanu ndikulapa zochimwa zanga Ndipo ndikupempha upangiri wanu ukhale nane. Mu mdzina la Yesu ndikupemphera, amen. Share this post, or copy and paste or simply type amen kuti wina wake lero lino apulumutsidwe ku moto wakugahena nalandira Yesu. Amen.
Posted on: Tue, 08 Jul 2014 14:50:01 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015