Nkhani yomvetsa chison: Malawi vsTanzania. Ambiri tadzutsa - TopicsExpress



          

Nkhani yomvetsa chison: Malawi vsTanzania. Ambiri tadzutsa mapirikaniro athu poganiza kuti nkhaniyi mwina ingakhale yamasewero a mpira koma ayi ndithu. Chakumma kwalero a Malawi okwana pafupifupi 32 omwe anali ku Tanzania aphedwa ndi asilikali adzikoli kamba kosemphana maganizo pankhani ya nyanja ya Malawi. Palipano ku Mzuzu anthu sakuloledwa kuyenda chifukwa asilikali adziko la Malawi ali paliponse. Ena mwa asilikaliwa apita ku Tanzania kukanyamula mitembo ya iwo amene aphedwa. Funso ndilakuti kodi zimenezi zikutanthaunji kumtundu wa a Malawi? Kapena ndi nkhondo ya a Ngitawo. Perekani maganizo anu okhwima bwino ndikuwagawira anzanu nkhaniyi. More updates to come.
Posted on: Wed, 25 Sep 2013 11:15:23 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015