Zina ukanva kamba ngati mwala chandibweletsa ku Malawi kuno - TopicsExpress



          

Zina ukanva kamba ngati mwala chandibweletsa ku Malawi kuno sindikuchidziwa koma chomwe chandichitikira ndinalandi call yochokera kumudzi yoti lachinayi ndipezeke ndili ku Malawi, pomwe ndidali kuntchito nthawi yomweyo mutu wangasunagwire mpaka ndapezekadi kuno ku Malawi, wadandaula chontcho nyamata ochokera mmudzi wa Chutira yemwe wakhala ali ku RSA munzinda wa Durban kwazaka 12 . Iye wati zikuonetsa ngati Makolo anga ndi omwe andipangila mankhwala kuti ndipezeke kuno opanda kalikose pamenepa olakwandani? Kholo kapena Mwana? #bundali
Posted on: Tue, 24 Sep 2013 10:34:22 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015