Austin amayangana nyumba yoti apange lend! akuyenda, anaona - TopicsExpress



          

Austin amayangana nyumba yoti apange lend! akuyenda, anaona post ina pa nkomo pa munthu wina kuti akupangisa lend nyumba. Austin anapanga odi ndipo abambo anyumba anatuluka: ndikuthandizeni? Austin: eyaah! Ndawelenga apo kuti muli ndi nyumba za lend? Abambo: eyaah! Tilinazo. Austin: mumapanga bwanji pa mwenzi? Abambo: mk2000! Austin: nanga chimbudzi zimakhala bwanji? Abambo: aaah osadandaula , Chibudzi ndi ulere ! Austin amvekele: oooh nkhani yabwino! Abambo: chifukwa? Austin: ndikupanga kale lend penapake ndipo ndikulipila mk 500 koma palibe chimbuzi,,,,nde ndipitiliza kukhala konko koma ndizizalowa chimbuzi chanuchi sinanga ndi ulere! A bambo anakomoka! #kabotolo#
Posted on: Tue, 26 Nov 2013 08:38:32 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015