BASITU,WAPITA MFANA UJA: Malinga ndi ma report kuchokera ku South - TopicsExpress



          

BASITU,WAPITA MFANA UJA: Malinga ndi ma report kuchokera ku South Africa, Gabadinho Mhango wakhonza mayeso ake ndi team ya Amazulu. Mkulu wa team ya Amazulu Japhet Zwane,watsimikiza kuti Gabadinho Mhango wapambana mayeso ake. Zwane wati Gabadinho Mhango amayenera kupimidwa ndi ma Dotolo mawa koma asintha ndipo pali chiyembekezo kuti Gaba apimidwa mawa. Zwane wati Gaba akuyenera kusaina contract ndi Amazulu kamba kakuti katswiriyu wagometsa Amazulu kumeneko. Zabwino zonse Gaba..... Timakunyadira,kapange zimene umadziwa zija......@Andy!!!
Posted on: Tue, 09 Jul 2013 20:49:47 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015