Chifukwa chake ine sindisata mpila wa ku #malawi ndiwochimwisa - TopicsExpress



          

Chifukwa chake ine sindisata mpila wa ku #malawi ndiwochimwisa heavy kuyambila ku ma #Club mpaka NATIONAL timu yonse ndi mbola. Malawi basi pitiliza zomwe umapangazo monga: •Kufula agalu •Kuphunzitsa ana ufiti •Kuba ndalama zakhani khani •Kugwirila ana kuwapasa matenda •Kulima chamba •Kubelekana ngati mchenga koma kulephera kupitisa Ana ku sukulu. •Kuzipopa kuti #ATUMBUKA amatha zonse monga zimenezi zoluzazi za ziiiiiii zeni zenii. •Kukhomelelana tokhatokha Zinazo mukuziziwa •Zandinyasa heavy musiye kumenya mpila mibwabwa inu shupiti koma kudya ndalama zaboma makolo a zigogo athu kumuziko kumavutika inu mukudya misokho yathu. Ndipo mibwabwa imeneyi akamazafika pa #KIA zawamphompholeni makofi guys kwa nonse mukukhala ku #Lilongwe FT : Algeria 3-0 mlw Mali 2-3 Ethiopia #mtimaKuwawaNdizampila
Posted on: Wed, 15 Oct 2014 21:27:48 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015