Eeish! guys, nzanga anafunsidwa funso ku ma intervew a Police(ORAL - TopicsExpress



          

Eeish! guys, nzanga anafunsidwa funso ku ma intervew a Police(ORAL INTERVEWS) The question sayz? can u tel us one duty of the Malawi police? My friend answered: to protect the president & the republic of Malawi. & they asked him again: How? Sananjenjemere koma kuyankha kuti: kumubereka(JB)Ku msana nkuthawa naye.ee naye ofunsa mafunso anagwa pansi ndi kuseka.kenako mnyamata anangoyankhula kuti , mmafuna kundiyesa eti? Kikikiki.
Posted on: Mon, 25 Nov 2013 20:04:17 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015