KOMA AKHALE WAULEMU NDI WOOPA MULUNGU!! Through inbox - TopicsExpress



          

KOMA AKHALE WAULEMU NDI WOOPA MULUNGU!! Through inbox ............................True story Adm tanditumizire pic yangayo komanso usabise dzina langaro chifukwa ndizasiliyasi Guys ndine Chaggie Chirwa kuno ku euthin ku Zimba munthune chifukwa choti ndikachoka kutchito ndimankhala nditatopa kwambiri komanso zomachapa ndekhazi ndatopa nazo ndafuna kupeza kumene kuli nthiti yanga woti ndizasungane nayo mpaka kale kotero iye amene asangalatsidwe nane asachite manyazi koma kungondi flasha pa number iyi 0888550724 ndipo ndimuyimbira pompo pompo osadandaula kuti eee nanga zovala kapena chani zonsezo ndinzamkonzera ndiineyo ngati mamuna wake chonde asakhale opitilira zaka 27 komanso akhale kuti ndiwaulemu maka mavalidwe komanso owopa mulungu.
Posted on: Sat, 24 Jan 2015 09:13:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015