MITIMA YOKONDWELA NDI UKULU WA MULUNGU PA MOYO WA PAPA J. Y. - TopicsExpress



          

MITIMA YOKONDWELA NDI UKULU WA MULUNGU PA MOYO WA PAPA J. Y. ZIBA We are trying to sechi mumaDikishonale kuti kodi Mau oyenera ndi ati kuchita refer to this amazing Man of GOD. Tiyeni tiwerenge zochepa izi zimene ena amene athandizika ndi Utumiki komanso Calling ya PAPA J. Y. ZIBA, Ministering Under Heavenly Mandate & Authority (osaiwala mau ofunikawa) anatitumizira kuno ku NN-Studios. Anthu akamakamba za mtsogolo kwa ine chinali chitonzo because I never knew & define what FUTURE is all about, but the day I met this Man anachotsa chigumato ndi chiseyeye chomwe chidachita dande mkamwa watsogolo langa ndikundininkha lomwe liri lowala ngwee tsogolo. Ndimachita matama lero kuti sindimadwala zimakhala ngati nkhamba kamwa, koma tsiku limene ndidachita mwai okhala pansi paUtumiki wao ndidali titabwera ndi mtenga-tenga wamatenda. Kuyambira Malungo, TB, Cancer, zotupa, ndidali play field yamatenda. Ndidamva ndikukhulupilira kuti whoever is in CHRIST, indeed is a New Creation zakale zavaya zatsala za Brand new. Anandisitika manja awo, omwe ali Bomag yosalazira ma potholes achifwilimbwiti ya nam’goneka wa Matenda. Lero nkamati ndidachita bid farewell to sickness, Don’t get surprised ndi PAPA J.Y. ZIBA production pantchito mwaine. Ndikakumana ndi Matenda chifukwa choti iwo aphonya njira yodutsamo yawo, *AMANGODZIWIRATU* Shuuuuuuuuuuuuuuuu!!! If you are praying close to meet, you’ll hear beautiful Language of the HOLY-GHOST, sindinali chonchi m’mene ndimakumana ndi MECHANIC wa Mkuluyu. Ndidali Blank kuposa Blank Disiki, ndidali mulendo ku Dziko la Uzimu kufikira atatenga Nyundo, Masipanala, Jeke, Lubricant Oils ndikundigumbutula ngati theyala m’manja wa tire fitter. Anandichita drain Oil wakale yense wachipembedzo ndikundikwecha ndikundithira Oil watsopano atatha kusintha ma spare adzimbiri amene amachita phokoso moyo wanga. Lero ndi Ine Prayer Minister, Nanga kopanda PAPA J. Y. ZIBA kuyankha INDE NDITUMENI kwa AMBUYE ndikadakhala Otani??? Ndikaima kuchipatala, pa College, University, m’Bus, ingakhale kumortuary ndikupantha Gospel anthu amabaizika kuti kodi Baibulo akuwelenga Mtumikili ndilomwe tagwira M’manja mwathuli? Kuli kuya kwamamvetsetsedwe a Baibulo (akuiwala kuti ndinabadwa nalo limodzi). Sindimathera pompo ndikamaliza kuwakwecha ndi Mau ndimawayalanso manja kuthamangitsa nsabwe komanso aphata onse omwe satana anawaika, kupemphelera odwala ndimamalizira kuzutsa anthu akufa ku mortuary. Ndimayenda ndikumaziyankhula kuti I hate Porverty, sikuti ndichifukwa choti ndinabadwira ku MW, koma ndikugwilizana ndi DIVINE Will pa moyo yomwe PAPA J. Y. ZIBA aitsitika monga nsoko pa uniform yawa police. Kukhala kulephera kunathawa nditamva za Wisdom that GOD gave Solomon & what is available to me now (CHRIST’s has become my Wisdom) I DON’T FAIL (It’s my Daily talk) Ngati muliponso ena kunjako amene banja, sukulu, moyo wanu wauzimu siukuyenda, musazimane bwerani kwa PAPA J. Y. ZIBA- Builder dyamkulungwa azagwetsa foundation ndizipupa zong’ambikazo ndikukweza zatsopano kupyolera M’mau AMULUNGU ndi KUDZODZA kwa MZIMU oyera. Ife anzanu tikusimba lokoma. I’m built on the word of TRUTH & My FAITH is the FAITH of CHRIST. Hahahahahahahahahahaha!!!!! SINDIINE MWAMASEWERATU!! Zama spiritual husbands & wives timamva kwa anthu ena, ife AYI ndithu mtendere okha-okha (JAN-DEC) & atheramonso sazafika kwathu. Atero Ambuye or prophesy to me mmmhhhh sadandiuzeko anangondiphunzitsa kuti in NEW Testament JESUS left Disciples NOT Prophets monga ziliri panomu ngati business yazitumbuwa…kikikkkkkkikikikkkk Sindifuna munthu wina kuti andiyankhulira kwa Abambo wanga, hehehehehe the same with ujeni…..aaahhhh mkazi wako, siumamupempha mnzako kuti akuchitire kiss & @ the end ufunse kuti kiss-yo amamveka bwanji Hahahhahahahahahaha Pwepweepweeeee!!!!! It’s one on one with our FATHER. Ndimve ndekha basi, ngati angawayankhule a pulofetiwo nanenso angandiyankhule basi aah!!! Ndi Chipangano chatsopanotu ichi hihihihihihihihihihihiii!!
Posted on: Wed, 24 Jul 2013 08:09:12 +0000

Trending Topics



">
About 7 years ago I was diagnosed with being a Highly Sensitive

Recently Viewed Topics




© 2015