Ndan amene safuna kukhala dokotala hahaha nyamata wina wa ku - TopicsExpress



          

Ndan amene safuna kukhala dokotala hahaha nyamata wina wa ku ndirande wagwidwa kuno stethoscope ili mu khosi,anthu amawadabwitsa daily amabwera Ku qz mamawa dzovala zommwe zomwezo kumagooneka ma corridor. Lero madokotala akuru Anamuwerenga kumufusa muli department iti akut department ya midwife office yanga ili kumusi hahaha,,,anakadziwa nkudzamufusaso chili mukhosich dzina lake nchan akut trescope ...,hahahahq koma ya anagomuyitanira alonda akut amangen awa ndi akuba...
Posted on: Thu, 14 Nov 2013 14:01:56 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015