ZIDAKWA ZAZIKULUZIKULU 10 MU CAPETOWN. #president george - TopicsExpress



          

ZIDAKWA ZAZIKULUZIKULU 10 MU CAPETOWN. #president george Mzwale,uyu ndi madala,amamwa mowa modabwitsa,mwana wake weniweni atamwalira iye anakatengapo ndalama zachipepetso ndikukamwera kusiya ntembo nyumba,amachokera ku sanga,vitekete(nkhota-kota) Vice president #mbewu,uyu amakhara ku lowa,anabwera kuno Mchaka cha 20002,ndalama yayikulu anatumizapo kumudzi ndi R50(fifity Rand) anatumiza chaka cha 200 9 amachokera kumatete(nkhata-bay) #inspector general philimon,uyu akalezera amayimba njira yotse nyimbo yoti sagona ndimumphwetekakwinaku atanyamura buluku Mmanja,kenako amatseka yekha mphwete,akafika pa nyumba amalira ngati kwagwa maliro,amachokera ku Mzimba. #minister of justice-harry chimutu,uyu amaneneratu kuti alikuno kutheba kuzathana ndi mowa,salary yake imathera pa mowa,anachita kupanga time-table yamowa,amachokera ku kaongozi. #SERGEANT-come joburg balaka,uyu ngakhale mpira kapena chilichotse pa Tv,saonelera amaonelera programme yekha yamalondo amowa,amakhara ku blackheath. #captain-Alfred chechalito-sambowa,uyu amachita kugona ndi mowa kumutu,amadzuku 1usiku ndikulawapo,anthu anachita kumuitana ndi dzina loti sambamowa #medical detective-julious kamanga,uyu akamwa,amazinyelera ndikuzikozera,anthu amachita kunyamura ngati maliro. #major general-isaac kalikote,uyu anamwera ndalama zamaliro ankazi wake,ngakhale 2koloko utsiku ngati kulimowa amatha kuyenda ntunda wautali.amachokera ku mwaya(nkhata-bay) #commanda-vincent chinemba,uyu ananeneratu kuti Mulungu wake osunga moyo wake ndi mowa,akamamwa amayamba ndi pemphero,iye amati chonde ambuye,tizimwa ndalama zisathe,ambuye sisani ntengo wa mowa-amachokera ku vitekete(nkhota-kota) izi ndizidakwa zazikuluzikulu mu capetown,zoti zimamwa every-day,tazakhalenitso pompo week ya mawa pomwe tizakupasileni Top 10 ya anyamata omwe amamwa kwambili jive ndi magwinya. NO FEAR NO FAVOUR. If u cant beat us,join us!! ZOCHITIKA PA CAPETOWN
Posted on: Mon, 26 Jan 2015 06:50:36 +0000

Trending Topics



margin-left:0px; min-height:30px;"> This is a journey I traveled with my late husband, Joe and this
I feel dat im not da perfect man dat I ought 2 be. Da reason y is
Cuando Mike Wazowski tenia seis años , visito con su clase
Traversing the Wall by Ramón Blanco (ARTifariti 2011) has been
Operation Executive Location:Ubi Working hour: 900am -
Savona: Presentazone del XXIII corso di introduzione alla
It was the least I could do since our continent abounds with over
Tipsa gärna unga i din omgivning om denna bra sak som händer på
From Ericlee: On Wednesday, we traveled to Stanford to get a
† Don’t Argue With God † Death and life are in the power

© 2015