Tikamati Malawi timanena Inuyo Nanga mukhala bwanji atsogoleri - TopicsExpress



          

Tikamati Malawi timanena Inuyo Nanga mukhala bwanji atsogoleri amawa.. 1 uhule kuli kudya kwanu(muzaramulira dzikoli mukudwala) 2 muzaramulira dzikoli mutapenga chamba mukusutacho 3 mudzakhala bwanji atsogoleri amawa Mukuba 4 Muzakamba bwanji zakumwamba mukutukwana ena Ife kwathu kwatha Tinazara mitengo ndiyoo Mukuonongayoo Malo moti mukadula mudzalemo ina Inu ayi Kwathu tinapanga kwatsala kwanu
Posted on: Tue, 13 Jan 2015 15:16:14 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015