admin hide my id. chonde atsikana anzanga mukukondani pilizi - TopicsExpress



          

admin hide my id. chonde atsikana anzanga mukukondani pilizi musadzayelekeze kupanga chibwenzi ndi mnyamata pa fb pano, eeeish anyamata ndiatambwali mapeto awa, ine ndinapanga chibwenzi ndi mnyamata wina wake pa fb ati anali pa chanco komanso ati amagwira ku airtel. eti wangondivula vula basi ndunena pano wandiblocker, ndafufuza zaonetsa kuti amagwira ntchito mu shop yamwenye mu limbe. koma ndanzimvera chisoni ine. you boys God will punish u.
Posted on: Wed, 20 Nov 2013 17:05:27 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015